-
Machitidwe 27:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako tinayamba kuyenda mʼmbali mwa chilumba china chachingʼono chotchedwa Kauda chimene chinkatiteteza ku mphepo. Komabe tinkalephera kuwongolera bwato lalingʼono limene ngalawayo inkakoka.
-