Machitidwe 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno atakweza bwatolo mʼngalawa, anayamba kumanga ngalawayo ndi zomangira kuti ilimbe. Ndipo poopa kuti ngalawayo ingatitimire mumchenga ku Suriti,* iwo anatsitsa zingwe zomangira chinsalu cha ngalawa moti inkakankhidwa ndi mphepo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:17 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 207 Galamukani!,10/8/1996, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, tsa. 245/15/1990, tsa. 26
17 Ndiyeno atakweza bwatolo mʼngalawa, anayamba kumanga ngalawayo ndi zomangira kuti ilimbe. Ndipo poopa kuti ngalawayo ingatitimire mumchenga ku Suriti,* iwo anatsitsa zingwe zomangira chinsalu cha ngalawa moti inkakankhidwa ndi mphepo.
27:17 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 207 Galamukani!,10/8/1996, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, tsa. 245/15/1990, tsa. 26