-
Machitidwe 27:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Titaona kuti dzuwa komanso nyenyezi sizinaoneke kwa masiku ambiri komanso tikukankhidwa ndi chimphepo champhamvu, tinayamba kukayikira zoti tipulumuka.
-