Machitidwe 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthuwo atakhala nthawi yaitali osadya kanthu, Paulo anaima pakati pawo nʼkunena kuti: “Anthu inu, mukanamvera malangizo anga, osachoka ku Kerete kuja, sitikanavutika chonchi komanso katundu sakanawonongeka.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:21 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 207-208
21 Anthuwo atakhala nthawi yaitali osadya kanthu, Paulo anaima pakati pawo nʼkunena kuti: “Anthu inu, mukanamvera malangizo anga, osachoka ku Kerete kuja, sitikanavutika chonchi komanso katundu sakanawonongeka.+