-
Machitidwe 27:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Komabe musadandaule chifukwa palibe amene ataye moyo wake, koma ngalawa yokhayi iwonongeka.