Machitidwe 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 nʼkunena kuti: ‘Usaope Paulo. Uyenera kukaima pamaso pa Kaisara.+ Ndipo dziwa kuti chifukwa cha iwe, Mulungu apulumutsa anthu onse amene uli nawo pa ulendowu.’ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2016, ptsa. 15-16
24 nʼkunena kuti: ‘Usaope Paulo. Uyenera kukaima pamaso pa Kaisara.+ Ndipo dziwa kuti chifukwa cha iwe, Mulungu apulumutsa anthu onse amene uli nawo pa ulendowu.’