-
Machitidwe 27:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Pa usiku wa 14, mphepo inayamba kutikankhira uku ndi uku panyanja ya Adiriya. Ndiyeno pakati pa usiku, oyendetsa ngalawayo anayamba kuganiza kuti akuyandikira kumtunda.
-