-
Machitidwe 27:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Choncho anayeza kuzama kwa nyanja nʼkupeza kuti inali mamita 36. Atayenda kamtunda pangʼono anayezanso kuzama kwake nʼkupeza mamita 27.
-