-
Machitidwe 27:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Tsopano oyendetsa ngalawayo ankafuna kuthawamo. Choncho anatsitsira bwato lija panyanja ponamizira kuti akufuna kutsitsa anangula kutsogolo kwa ngalawayo.
-