Machitidwe 27:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Paulo anauza mtsogoleri wa asilikali ndi asilikaliwo kuti: “Anthu awa akachoka mʼngalawa muno, simupulumuka.”+
31 Paulo anauza mtsogoleri wa asilikali ndi asilikaliwo kuti: “Anthu awa akachoka mʼngalawa muno, simupulumuka.”+