-
Machitidwe 27:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Kutatsala pangʼono kucha, Paulo anayamba kuuza onse kuti adye. Iye anati: “Tsopano patha masiku 14 mukudikirira komanso muli ndi nkhawa ndipo simunadye chilichonse.
-