-
Machitidwe 27:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Atanena zimenezi, anatenga mkate. Kenako anayamika Mulungu pamaso pa onse nʼkugawagawa mkatewo ndipo iye anayamba kudya.
-