Machitidwe 27:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kutacha, sanadziwe kuti ali kuti,+ koma anaona gombe linalake lamchenga ndipo ankafunitsitsa kuti ngati nʼkotheka akaimitse ngalawa pamenepo.
39 Kutacha, sanadziwe kuti ali kuti,+ koma anaona gombe linalake lamchenga ndipo ankafunitsitsa kuti ngati nʼkotheka akaimitse ngalawa pamenepo.