-
Machitidwe 27:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Choncho anadula zingwe za anangula nʼkuzigwetsera mʼnyanja. Anamasulanso zingwe zomangira nkhafi zowongolera. Atakweza mʼmwamba nsalu yakutsogolo ya ngalawa, anayamba kulowera kugombelo.
-