-
Machitidwe 27:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Kenako anafika pachimulu cha mchenga chomwe mafunde ankachiwomba mbali zonse. Kutsogolo kwa ngalawayo kunakanirira pansi mumchengawo osasunthika ndipo mafunde amphamvu anayamba kuwomba kumbuyo kwake moti inayamba kusweka zidutswazidutswa.
-