Machitidwe 27:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Zitatero asilikali anaganiza zopha akaidi kuti pasapezeke aliyense wosambira nʼkuthawa.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:42 Nsanja ya Olonda,5/1/1999, tsa. 30