-
Machitidwe 27:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Koma mtsogoleri wa asilikali ankafunitsitsa kuti Paulo akafike naye ali bwinobwino, choncho anawaletsa kuchita zimene ankafunazo. Ndiyeno analamula odziwa kusambira kuti alumphire mʼnyanjamo kuti akhale oyamba kukafika kumtunda.
-