Machitidwe 27:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Analamulanso ena onse kuti achite chimodzimodzi, ena pamatabwa ndipo ena pa zidutswa za ngalawayo. Pamapeto pake onse anafika kumtunda ali bwinobwino.+
44 Analamulanso ena onse kuti achite chimodzimodzi, ena pamatabwa ndipo ena pa zidutswa za ngalawayo. Pamapeto pake onse anafika kumtunda ali bwinobwino.+