-
Machitidwe 28:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma Paulo atatola nkhuni nʼkuziponya pamoto, panatuluka njoka ya mphiri chifukwa cha kutentha ndipo inamuluma nʼkukanirira kudzanja lake.
-