Machitidwe 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu achilankhulo chachilendowo ataona njoka yapoizoni ikulendewera kudzanja lake, anayamba kuuzana kuti: “Ndithu munthu uyu ndi wopha anthu chifukwa ngakhale kuti wapulumuka panyanja, Chilungamo* sichinamulole kuti akhalebe ndi moyo.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:4 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 210 Nsanja ya Olonda,10/1/2015, tsa. 95/1/1999, ptsa. 30-31
4 Anthu achilankhulo chachilendowo ataona njoka yapoizoni ikulendewera kudzanja lake, anayamba kuuzana kuti: “Ndithu munthu uyu ndi wopha anthu chifukwa ngakhale kuti wapulumuka panyanja, Chilungamo* sichinamulole kuti akhalebe ndi moyo.”