-
Machitidwe 28:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Pafupi ndi malowa, panali minda ya munthu woyangʼanira chilumbacho, dzina lake Papuliyo. Iyeyu anatilandira bwino kwambiri ndipo anatichereza kwa masiku atatu.
-