Machitidwe 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma bambo ake a Papuliyo ankadwala malungo* komanso kamwazi ndipo anali chigonere. Choncho Paulo analowa mmene bambowo anali nʼkupemphera ndipo kenako anawagwira pamutu* nʼkuwachiritsa.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:8 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 210
8 Koma bambo ake a Papuliyo ankadwala malungo* komanso kamwazi ndipo anali chigonere. Choncho Paulo analowa mmene bambowo anali nʼkupemphera ndipo kenako anawagwira pamutu* nʼkuwachiritsa.+