Machitidwe 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero, anthu ena onse amene ankadwala pachilumbacho, anabwera kwa iye ndipo anawachiritsa.+