-
Machitidwe 28:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Patapita miyezi itatu, tinanyamuka pangalawa ya ku Alekizandiriya yokhala ndi chizindikiro cha “Ana a Zeu.” Ngalawa imeneyi inaima pachilumbapo poyembekezera kuti nyengo yozizira ithe.
-