-
Machitidwe 28:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Titachoka kumeneko, tinazungulira nʼkukafika ku Regio. Patatha tsiku limodzi, kunayamba kuwomba mphepo yakumʼmwera ndipo tsiku lachiwiri tinafika ku Potiyolo.
-