-
Machitidwe 28:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Iwo anamuyankha kuti: “Ife sitinalandire makalata alionse ochokera ku Yudeya onena za iwe. Palibenso aliyense wa abale amene afika kuno, amene watiuza kapena kulankhula choipa chilichonse chokhudza iwe.
-