Machitidwe 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe tikufuna kumva maganizo ako, chifukwa kunena zoona, ife tonse timadziwa kuti gulu lampatuko limeneli+ amalinenera zoipa kwina kulikonse.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:22 Nsanja ya Olonda,2/15/1994, tsa. 57/1/1993, ptsa. 5-6, 15
22 Komabe tikufuna kumva maganizo ako, chifukwa kunena zoona, ife tonse timadziwa kuti gulu lampatuko limeneli+ amalinenera zoipa kwina kulikonse.”+