-
Aroma 1:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kalatayi ndalembera inu nonse okhala ku Roma amene mumakondedwa ndi Mulungu komanso munaitanidwa kuti mukhale oyera:
Mukhale ndi kukoma mtima kwakukulu ndiponso mtendere wochokera kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye wathu Yesu Khristu.
-