Aroma 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Enanu mumadzitchula kuti ndinu Ayuda,+ mumadalira Chilamulo ndiponso mumadzitama kuti muli pa ubwenzi ndi Mulungu.
17 Enanu mumadzitchula kuti ndinu Ayuda,+ mumadalira Chilamulo ndiponso mumadzitama kuti muli pa ubwenzi ndi Mulungu.