-
Aroma 2:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mumaganiza kuti mungathe kuwongolera anthu opanda nzeru. Mumaganizanso kuti mungathe kuphunzitsa ana chifukwa mumamvetsa komanso kudziwa choonadi chopezeka mʼChilamulo.
-