Aroma 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Dzina la Mulungu likunyozedwa pakati pa anthu amitundu ina chifukwa cha inu,” ngati mmene Malemba amanenera.+
24 “Dzina la Mulungu likunyozedwa pakati pa anthu amitundu ina chifukwa cha inu,” ngati mmene Malemba amanenera.+