Aroma 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho ngati munthu wosadulidwa+ akutsatira mfundo zolungama za mʼChilamulo, kusadulidwa kwake kudzaonedwa ngati kudulidwa, si choncho?+
26 Choncho ngati munthu wosadulidwa+ akutsatira mfundo zolungama za mʼChilamulo, kusadulidwa kwake kudzaonedwa ngati kudulidwa, si choncho?+