-
Aroma 2:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Munthu amene ndi wosadulidwa akamatsatira Chilamulo, adzakuweruza. Adzakuweruza iweyo amene umaphwanya Chilamulo ngakhale kuti uli ndi malamulo olembedwa ndiponso ndiwe wodulidwa.
-