Aroma 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma tsopano, zadziwika kuti munthu akhoza kukhala wolungama kwa Mulungu popanda kutsatira Chilamulo.+ Zimenezi zinatchulidwanso mʼChilamulo komanso zimene aneneri analemba.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:21 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 20
21 Koma tsopano, zadziwika kuti munthu akhoza kukhala wolungama kwa Mulungu popanda kutsatira Chilamulo.+ Zimenezi zinatchulidwanso mʼChilamulo komanso zimene aneneri analemba.+