-
Aroma 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mwachitsanzo, zikanakhala kuti Abulahamu ankaonedwa kuti ndi wolungama chifukwa cha zimene anachita, akanakhala ndi chifukwa chodzitamira, koma osati pamaso pa Mulungu.
-