Aroma 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu amene wagwira ntchito saona malipiro ake ngati kukoma mtima kwakukulu, koma ngati zimene amayenera kulandira.*
4 Munthu amene wagwira ntchito saona malipiro ake ngati kukoma mtima kwakukulu, koma ngati zimene amayenera kulandira.*