Aroma 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma Mulungu amene amaona anthu ochimwa kukhala olungama amaona kuti munthu yemwe sanagwire ntchito, koma amamukhulupirira, ndi wolungama.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2023, tsa. 3
5 Koma Mulungu amene amaona anthu ochimwa kukhala olungama amaona kuti munthu yemwe sanagwire ntchito, koma amamukhulupirira, ndi wolungama.+