Aroma 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiye kodi anthu odulidwa okha ndi amene amakhala osangalala choncho? Kapena osadulidwa nawonso amakhala osangalala?+ Popeza timati: “Abulahamu anaonedwa kuti ndi wolungama chifukwa cha chikhulupiriro chake.”+
9 Ndiye kodi anthu odulidwa okha ndi amene amakhala osangalala choncho? Kapena osadulidwa nawonso amakhala osangalala?+ Popeza timati: “Abulahamu anaonedwa kuti ndi wolungama chifukwa cha chikhulupiriro chake.”+