Aroma 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuti adzakhalenso bambo wa ana odulidwa, osati odulidwa okhawo, komanso wa amene amayenda moyenera potsatira chikhulupiriro chimene bambo wathu Abulahamu+ anali nacho asanadulidwe.
12 Kuti adzakhalenso bambo wa ana odulidwa, osati odulidwa okhawo, komanso wa amene amayenda moyenera potsatira chikhulupiriro chimene bambo wathu Abulahamu+ anali nacho asanadulidwe.