Aroma 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa Abulahamu kapena mbadwa* zake sanalonjezedwe kuti adzalandira dziko monga cholowa chawo chifukwa cha Chilamulo ayi.+ Analandira lonjezolo chifukwa chakuti Abulahamu anali ndi chikhulupiriro ndipo Mulungu anamuona kuti ndi wolungama.+
13 Chifukwa Abulahamu kapena mbadwa* zake sanalonjezedwe kuti adzalandira dziko monga cholowa chawo chifukwa cha Chilamulo ayi.+ Analandira lonjezolo chifukwa chakuti Abulahamu anali ndi chikhulupiriro ndipo Mulungu anamuona kuti ndi wolungama.+