-
Aroma 4:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Chifukwa ngati anthu amene akutsatirabe Chilamulo ndi amene adzalandire cholowacho, ndiye kuti chikhulupiriro chilibenso ntchito ndipo lonjezo lija lathetsedwa.
-