-
Aroma 4:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Nʼchifukwa chake iye anapatsidwa lonjezolo chifukwa cha chikhulupiriro, kuti likhale logwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu.+ Komanso anapatsidwa lonjezolo kuti likhale lotsimikizika kwa anthu onse omwe ndi mbadwa* zake,+ osati otsatira Chilamulo okha, komanso otsatira chikhulupiriro cha Abulahamu yemwe ndi bambo wa tonsefe.+
-