Aroma 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa ngati tagwirizana naye pofa imfa yofanana ndi yake,+ ndithudi tidzagwirizananso naye poukitsidwa mofanana naye.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2020, ptsa. 5-6
5 Chifukwa ngati tagwirizana naye pofa imfa yofanana ndi yake,+ ndithudi tidzagwirizananso naye poukitsidwa mofanana naye.+