-
Aroma 7:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndikulankhula ndi inu abale, amene mumadziwa Chilamulo. Kodi simukudziwa kuti Chilamulo chimakhala ndi mphamvu pa munthu pamene munthuyo ali ndi moyo?
-