-
Aroma 7:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Sinditha kumvetsa zimene zimandichitikira. Chifukwa zimene ndimafuna kuchita, sindizichita. Koma zimene ndimadana nazo nʼzimene ndimachita.
-