Aroma 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ngati muli ogwirizana ndi Khristu,+ mzimu umachititsa kuti mukhale ndi moyo chifukwa cha chilungamo ngakhale kuti thupi ndi lakufa chifukwa cha uchimo.
10 Koma ngati muli ogwirizana ndi Khristu,+ mzimu umachititsa kuti mukhale ndi moyo chifukwa cha chilungamo ngakhale kuti thupi ndi lakufa chifukwa cha uchimo.