Aroma 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngati mzimu wa amene anaukitsa Yesu uli ndi inu, iye amene anaukitsa Khristu Yesu adzachititsanso matupi anu omwe angathe kufawo+ kukhala ndi moyo,+ pogwiritsa ntchito mzimu wake umene uli ndi inu.
11 Ngati mzimu wa amene anaukitsa Yesu uli ndi inu, iye amene anaukitsa Khristu Yesu adzachititsanso matupi anu omwe angathe kufawo+ kukhala ndi moyo,+ pogwiritsa ntchito mzimu wake umene uli ndi inu.