Aroma 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 ndani adzawatsutsa? Khristu Yesu ndi amene anafa komanso ndi amene anaukitsidwa. Iye ali kudzanja lamanja la Mulungu,+ ndipo amatilankhulira mochonderera.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:34 Nsanja ya Olonda,10/15/2001, tsa. 14
34 ndani adzawatsutsa? Khristu Yesu ndi amene anafa komanso ndi amene anaukitsidwa. Iye ali kudzanja lamanja la Mulungu,+ ndipo amatilankhulira mochonderera.+