Aroma 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo ndi ana a makolo athu akale.+ Komanso Khristu anabadwa ngati munthu kuchokera kwa iwo.+ Mulungu, yemwe ndi wamkulu pa zinthu zonse, atamandike mpaka kalekale. Ame. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:5 Kukambitsirana, ptsa. 405-406
5 Iwo ndi ana a makolo athu akale.+ Komanso Khristu anabadwa ngati munthu kuchokera kwa iwo.+ Mulungu, yemwe ndi wamkulu pa zinthu zonse, atamandike mpaka kalekale. Ame.