Aroma 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe sizikutanthauza kuti mawu a Mulungu sanakwaniritsidwe. Chifukwa si onse omwe ndi mbadwa za Aisiraeli amene alidi “Aisiraeli.”+
6 Komabe sizikutanthauza kuti mawu a Mulungu sanakwaniritsidwe. Chifukwa si onse omwe ndi mbadwa za Aisiraeli amene alidi “Aisiraeli.”+